| Oh, Sispence, oh oh oh Ritaa.. Hello? (Verse 1) Munachoka kuti mukukasaka ndalama Mpaka lero simunabwelerenso Munachoka kutisiya ndi amai athu Koma simunabwelere.. Simumatumizanso chithandizo kunyumba Koma zoti mukuchita bwino tikumva Sitimadziwa ngati mumatiganizira Sitimadziwa ngati mumatikumbukira (Chorus) Mubwere kunyumba Mubwelere kunyumba Mubwere kunyumba Mubwelere kunyumba.. (Verse 2) Tinakula, otilera anali mai athu Kuvutika pamodzi ndi amai athu Komanso mutangopita, achimwene anatisiya Ana anu akungolira, Chilichonse kuvutikira Phone yokha mukanatiimbira (hello?) Kalata yokha mukanatilembera (you know) Sitimadziwa ngati mumatiganizira Sitimadziwa ngati mumatikumbukira (Chorus) Mubwere kunyumba Mubwelere kunyumba Mubwere kunyumba Mubwelere kunyumba (Bridge) Ohh, mubwelere kunyumba Oh, oh, oh .. Mubwelere kunyumba (Chorus) |
| Oh, Sispence, oh oh oh Ritaa... Hello? (Verse 1) You left, saying you're going to look for money, Till today You never came back You left us with our mother, But you never came back.. you don't even send any help back home, But we've heard you're doing so well We don't know if you think of us We don't know if you still remember us (Chorus) Come home Come back home Come home Come back home.. (Verse 2) We grew up, our mother raised us Struggling together with our mother And soon after you left, our brother died Your children are just crying, struggling with everything At least you could have phoned us (hello?) At least you could have written us ( you know?) We don't know if you think of us, we don't know if you still remember us (Chorus) Come home Come back home Come home Come back home (Bridge) Ohh, come back home Oh, oh, oh.. Come back home (Chorus)
Credits Song: Malawi folk song Artist: Ritaa (Rita Mwantalli) Text & translation: Lucky01 on lyricstranslate.com Music video: Courtesy of Ritaa Hosted by: Droomwevers World of Music - www.droomwevers.nl Copyright: Fair use principle, for educational purposes.
|